Kishore Kumar Hits

Leslie Moyo - Bambo A Tereza lyrics

Artist: Leslie Moyo

album: Nthambi


Bambo atereza chonde tisiyane bwino
Bambo atereza chonde tisiyane bwino
Ngati banja latha chonde tisakangane
Ngati banja latha chonde tisakangane
Ine ndizakwatila ndinunso kukwatila
Akakhala anawa awasunga Mulungu
Bambo atereza tisiyane bwino
Bambo atereza tisiyane bwino
Musandichitise manyazi iiih
Mowa mowa monse mwayambila
Kugona kunja osaleka
Akazi nawo osayamba
(Oooh no no no)
Mwamanga manyumba moyenda
Ndikomwe ma night anu muma spenda
Mmmmh nanu mukuchulusa zokamba bwanji
Ulendowo osangowuyamba bwanji
Monse mwayambila pokopoko
Pamaso pamikoko yogona akutame ndani
Pakhomo pako ndima spenda
Tsiku lonse olo goma osamenda
Ulesi thoo
Phindu lako ndi chani
Ndi bwino ndisale ndi tereza amayi nyamukani
Iyaaa
Bambo atereza chonde tisiyane bwino
Bambo atereza chonde tisiyane bwino
Ngati banja latha chonde tisakangane
Ngati banja latha chonde tisakangane
Ine ndizakwatila ndinunso kukwatila
Akakhala anawa awasunga Mulungu
Bambo atereza tisiyane bwino
Bambo atereza tisiane bwino
Mmmmh yes i got you right
Tingosiyanapo with no fight
But every day and night
Achina tereza see us fighting right?
Mmmmh lero limenero
Muoneke wabwino kamba pali makolo
Zayangana ku ngolo
Katundu ndi uyo akukunyamulizani ankolo
Ndiwe mamuna otani
Ubwino wanga siuyamika
Tinabereka ana ana
Kodi ulibe chisoni
Oooh amama ndanongoneza bondo
Bola ndikanangonena toto
Uyu si mamuna uyu
Phunotu salota uyu
Bambo atereza chonde tisiyane bwino
Bambo atereza chonde tisiyane bwino
Ngati banja latha chonde tisakangane
Ngati banja latha chonde tisakangane
Ine ndizakwatila ndinunso kukwatila
Akakhala anawa awasunga Mulungu
Bambo atereza tisiyane bwino
Bambo atereza tisiyane bwino
Mmmmm yes i got you right
(Tisiyane bwino)
Mmmmm,yes i got you right
(Tisiyane bwino)

Поcмотреть все песни артиста

Other albums by the artist

Similar artists