Kishore Kumar Hits

Charisma Madness - MABODZA - remix lyrics

Artist: Charisma Madness

album: MABODZA (remix)


Koma boy's sizoonayi
Henwood mhu mhu mhu
Ase Trappy
Mwana bad man
Bad we de remix, (ah yah yah yah yah yah)
You know waguan, (too ghetto too gutter)
Its for da gin
Yeah uh
Ndukupalani mamba mafana
Mumathamanga pakamwa
Kukamba za ineyo
Mpaka kutsamwa
Munandidilitsapo panopa ndinazama
Ukukayikira pita kafuse Anagama
Lupanga pansi pa mphasa ndimagona pa bed
Bawa chi penalty, ineyo ndi Mabedi
Ati ndimakonda chani
Ndawauza ma babe
Ine ndichi Martse
Mphwanga sungandivetse
Hit after hit ngati mfana wa boxing
Ndiku runner game, mafana you jogging
Amkati ndine mfana uh, you joking
Mukundi browser be, now you stalking
Amkati ineyo ndi mfana
Mabodza
Chaka chino nde chi changa ine
Mmanama
Yah yah yah yah yah yah yah
Amkati ineyo ndi mfana
Mabodza
Chaka chino nde chi changa ine
Mmanama, (heeeee)
Yah yah yah yah yah yah yah
Amkati ndimayimba zong'aza
Sinza hitter
Ndine mfana osatha kucheza
Sinzapita
Ndizingokhalabe pompaja
Ngati apaka glue
Amkangondikambilana akakhala paka gulu
Amvekele Czar uja nde samatha
Sangavaye kulikose atha ngati ada aja
Wangobwela kudzayesa zida akudoja
Mumuona 2021 atagonja
Mumanama mukuona zomwe ndikupangazi
Ine ndikupanga dzina inu mukupanga zi
Mukulimbana ndi beef, odi mchotse dalazi
Ati Czar ndi wamisala, zopangira dala zi
Yah, musama swethe nane
Ndimadya thukuta langa, adad
Nonsenu ndinu ana anga
Ndimagetsa zi ma hit
Ndine chiphinjo ndimabwera nzi ma verse
Ndine mkulu wa mpingo
Ndimatha kumenya nyimbo imodzi chaka chonse
Komabe ndikunveka heavy chaka chonse
Uona tima hater tanga tadaka tose
Ti akazi tomwe mumafila ndaphaka tonse
Mwana osatha kukwa, ndimayendachokhala
Pano uwu handsome ndi mthumba
Ndili ndizima looks
Pano ndimadya bafa
Mkana sindi spitter dirty
Ndimadya rapper, kumusiya kulichete
Amkati ineyo ndi mfana
Mabodza
Chaka chino nde chi changa ine
Mmanama
Yah yah yah yah yah yah yah
Amkati ineyo ndi mfana
Mabodza
Chaka chino nde chi changa ine
Mmanama, (yoo achina G-A)
Yah yah yah yah yah yah yah, (yoo)
Yoh rise up ghetto youth
Nthawi yo huster asakupatse tchuthi
Mfanawa amafuna ukhale m'musi
Samasangalala uka riser ngati vu
Koma ndiwafinya battery lo
LIli full ndilisiya battery low
Yo crew yanga siyama boss
Ndi bad company ndupanga loss
Heh ndungobwera ndima punch
Fungo la usipe nanga udzimanilanji
Ndine mfana ovaya heh
Mfana woyaka too much
Chifukwa ndi beef ndiya braz
Ineyo mfana bodza
Kapena amalota
Samadziwa ndimasungiratu nyota uh
Kungolimbika kunyoza
Chilichose ndimagwira ndima conquer
Mfuna Jane around mkazi wachikoka
Kungomwyata silent osafooka
Monday kungowona P-S but now you can't own her
Chi babes ichichi ndichi deal
Mood all day baby you can call it real
Lilime lili swift i just shoot to kill
Sindikusuntha inetu ndi mwini film
Amkati ineyo ndi mfana
Mabodza
Chaka chino nde chi changa ine
Mmanama
Yah yah yah yah yah yah yah
Amkati ineyo ndi mfana
Mabodza
Chaka chino nde chi changa ine
Mmanama
Yah yah yah yah yah yah yah
Eh, i'm high as my feature fee
You'll get hyped up off the greenery
It's all thumbs koma it's never been visa V
See we at the top stupid it's a different scenery
I'm king resonant mob if you disagree
I see no arm like a missing limb
I've been stylish rapper shetin' calligraphy
I'm rapping with fans every session is a meet and greet
Ngini iyi yokha ndinazama
Kutafuna ma beat oti mukhoza kutsamwa
Mukumanga malamba ifeyo tinavaya
Simudabwa ma guy ma collabo amandiswaya

Поcмотреть все песни артиста

Other albums by the artist

Similar artists