Link up Link up Link up Can we link up Ubwere ndi zi kush ndizi liquor Ubwere ndi anzako timenye drink up Titha kufika mawa ngati mukulimba Ti blowe cash ti blowe kush ti blowe shisha Patricia ndi jesse koma osati lingard Way she wine ngati glass ya linga Koma sungamkwere ngati mtengo wa minga Ndi oopya heavy deni ya msing'anga Nfana oyela heavy ngati zi mkaka Takin shots after shots mpaka ndi blacka Gist ili ball apa ndimaka She make man a go mushy Amashala chaku ku north ngati zephyr Zodiac sign ndika leo ngati lev Zambian girls ati ndili mushe Link up Ubwere ndi zi kush ndizi liquor Ubwere ndi anzako timenye drink up Titha kufika mawa ngati mukulimba Ti blowe cash ti blowe kush ti blowe shisha Can we link up Ubwere ndi zi kush ndizi liquor Ubwere ndi anzako tizamenye drink up Titha kufika mawa ngati mukulimba Am the coolest kid in malawi Kamuzu banda wangozaza mu baggie Rose chiwambo ango twerka ngati cardi Chilembwe ndi bingu ango fila ku side b Ubwere ndi nzako tizamenye 3 some Kuziwakale deal nde dinculm Life is too short when you having fun Moti apapa ikutsika mmene ukundi kissa mu Mad love from chitipa to nsanje Straight from africa thats malawi Egyptian ting how am rolling with mummies Sweet like candy wine fi daddy She a baddie og she dont copy nobody 265 mdubs to the world Link up Ubwere ndi zi kush ndizi liquor Ubwere ndi anzako timenye drink up Titha kufika mawa ngati mukulimba Ti blowe cash ti blowe kush ti blowe shisha Can we link up Ubwere ndi zi kush ndizi liquor Ubwere ndi anzako timenye chi drink up Titha kufika mawa ngati mukulimba