Yeah yeah yeah yeah Mmm Yeah yeah yeah yeah Yeah yeah yeah yeah Mmm Yeah yeah yeah yeah Yeah yeah yeah yeah Mmm Yeah yeah yeah yeah What Monalisa ati wandi missa Akangondipeza akuti andi kisser Angellina akungo beepa Akuti ndivaye kwawo wagula zi liqour Tinah eh wachimbina Kuthamangila kwathu wachoka chosimphina Mnachita kulembalana schedule ndi christina Umaziwa mariobro gang ndiyokhwithima Tili momo ngati chisomo Tili momo ngati chisomo Tili momo ngati chisomo Tili momo ngati chisomo Tili momo ngati chisomo Kiss ting ndiya milomo Punchline ndiya mikono Sick ting siya regional Tapiwa ndi yacinta Ati amafila zomwe ndimaimba Addicted to my sound amachita kumwera syrup Wagula 10 copies ya chamba cha hiphop Okay okay okay jane ama leaner Okay den sama cleaner Amadana ndi zamaina Aku charger mtengo wa malaina Nanga anitta, josophine, maryjane Chisomo nde ukuziwa kuti ali momo kale Kulowa olo popanda space kuzi squiza Ndimahita baby mama memory card ya nyimbo kale Melissa yacinta onse ali mkati ngati panti Kukonda wachi mbina olo flat Tili momo ngati chisomo Tili momo ngati chisomo Tili momo ngati chisomo Tili momo ngati chisomo Jane, linda, serena, melina Grâce, scillah, vanessa and vanilla Yo tili momo ntill the end Kugula puma kuti ndipange Right back ngati trent Kulowa stu kuti ndidrope trend Pull up muchi vroom Kuchotsa v andipeze room It's too big ngati zoom Point blank ndichi tune Ah ah ah shit Am ghetto and handsome nigga Kukonda chi figure working on numbers like Am bensam nigga via chinsapo chaku Likuni ku tchila ndi texam nigga Kuvungira cross kuti ikupatse head Ine ndi beckham nigga Kuthila gas kulowa ntown tipange grease Ndavaya ndekha koma pobwera, kubwera ndi gs Gs izizi, piss enemies Dash overseas, shaker nyash to me please Please bitch please Tili momo Tili momo Tili momo Tili momo Tili momo Tili momo Tili momo Tili momo