It's Driemo ooh Is this a joke? Are you kidding me? Utanthauza chani? zachuluka ndi nkhani You're planning to leave me Am I a fool? For falling for you Tadutsa muzambiri, tapangadi zambiri Now you want to switch like that Oh, kodi ndayipa pano Ndakubowa pano Zonse zija wandichititsa zikayipe pano? Oh kodi ndayipa pano oh Ndakubowa pano eh Zonse zija unandiphunzitsa zikayipe lero? Unandiyambitsa shisha, mowa mesa ndiwe? Iwe na-ine muma club everyday Lero ukuti khalidwe la banja mwa Ine mulibe Kodi ndi game ya mtundu wanji you are playing? Nde unkandisinthira? sinthiranji Nde unkandisinthiranji? oh my God Ine Fees yako itashupha ndinagulitsa munda Ine Lero munagwidwa ndi shasha, ati ine ngwa kumunda oh Koma izizi ndimkapanga chifukwa ndimasamala za ife Ineyo ndinka blander kufuna kukusangalatsa iwe How I wish I could go back (go back) How I wish I could rewind How I wish I could fall back (fall back) But It's too late (too late) Poti ndayipa pano (pano) Ndakubowa pano (pano) Zonse zija unandiphunzitsa zikayipe lero? Unandiyambitsa shisha, mowa mesa ndiwe? Iwe na-ine muma club everyday Lero ukuti khalidwe la banja mwa Ine mulibe Kodi ndi game ya mtundu wanji you are playing? Nde unkandisinthira? Zomwe mutandisiyile pano Zomwe mudandiphunzitsa Zomwe mutanditukwane nazo pano Ndi zomwe mudandidziwitsa Unandiyambitsa shisha, mowa mesa ndiwe? Iwe na-ine muma club everyday Lero ukuti khalidwe la banja mwa ine mulibe Kodi ndi game ya mtundu wanji you are playing? Nde unkandisinthira? How I wish I could go back How I wish I could rewind Fall back, but It's too late (too late)