Kukumazizila kukada, Tsiku kuchedwa kutha kukacha tsiku lonse mvula mawawa. simngachedwe ndidziwe zamawa
Mano anga anthu sawaona
Sikweni kweni kusekelera
Usiku zindivuta kugona
ngati udzudzu ndimachezela
Moyo wathu dzana umkakoma
kachikondi kutsekemera
Ubwino kukoma opanda phuma
kachikondi kulemelera
Alipo akukonda
Alipo akukuhoda
Alipo akukugwila
ndikungoganizira eeya
alipo akukuuza amakukonda kuposa ine ee
Poti dziko langa likuzizira popanda iwe ee
Chikondi chinali on point,
ngati nyimbo yolondola ma note.
Chinali perfect chinalibe fault
Anthu okamba amkati tili hot
Zoti chikondi chimawawa inali mphekesela, anthu ena akamakamba ndimkangomvetsela
anthu amkatopa kusowa chotigwetsela
Komalero tandiona ndingo fwethela
Maso anga ayandama in tears
Mtima wanga udzadza ndi fear
Usaganize zoti usiye,.ndikungoganizira
Alipo akukonda
Alipo akukuhoda
Alipo akukugwila
ndikungoganizira eeya
alipo akukuuza amakukonda kuposa ine ee
Poti dziko langa likuzizira popanda iwe ee
Poti chikondi mnakupatsa chija nchokwanira
kuti udzadikila mpaka mthawi idzakwanila
mkhale mutu utaotcha udzakakamira
chikondi chako chikuthawa kodi udzambwandila
ndiwe wekha ndikufuna mdziko langa dear
mtima wako usakaike ndiwe wanga dziwa
ndipephero langa mthawi zonse kuti kwaiwe wekha ndiko mtima wanga ugundila
Alipo akukonda
Alipo akukuhoda
Alipo akukugwila
ndikungoganizira eeya
alipo akukuuza amakukonda kuposa ine ee
Poti dziko langa likuzizira popanda iwe ee
Alipo akukonda
Alipo akukuhoda
Alipo akukugwila
ndikungoganizira eeya
alipo akukuuza amakukonda kuposa ine ee
Poti dziko langa likuzizira popanda iwe ee
Поcмотреть все песни артиста
Other albums by the artist