Oh, oh-oh (Abstract) Hmm-hmm-hmm, mm-mm Mayi inuyo anakonza Nde zoti wina azikuseweletsa kwa ineyo sizoona Nde mukuzuzikiranji mayi wokongola ngati inu, ngati inu? Nde ukunzunzikiranji mkazi wokongola ngati iwe (mkazi wokongola ngati iwe) Mamuna wako ndi wa nsanje Usakhale pa phone ati akuyankhulana ndinda? Oh, whooh Sizimuwaza ukakhala ndi anzako Amawopa akuwuza chilungamo Zomwe amachita iwe kulibeko Ichichi si chikondi, you have to let go Nde umayenera chikondi chosefukira, kira Nde ukamalira pansi pa mtima uzidziwa Kuti uli ngati duwa Akusamale, akuthilire uwale Mayi inuyo anakonza (huh) Nde zoti wina azikuseweletsa kwa ineyo sizoona Nde ukunzunzikiranji mkazi wokongola ngati iwe (mkazi wokongola ngati iwe) Mkazi wokongola ngati iwe (mkazi wokongola ngati iwe) Nde ukunzunzikiranji Nde ukunzunzikiranji Mm-mm Oh, oh-oh Ooh, ooh-ooh (oh-oh-oh) Mm-mm-mm, mm-mm Sungamusinthe ndim'mene aliri Anayesapo ena zinavuta nde usakhalire kukhetsa misonzi Amuna abwino aliko Kungotaya nthawi Is he even worth it? Akuwuseretsa mwayi Zochita zake ndi zogwetsa mphwayi Umayenera chikondi chosefukira (kira) Nde ukamalira pansi pa mtima uzidziwa Kuti uli ngati duwa Akusamale, akuthilire uwale Mayi inuyo anakonza (ah) Nde zoti wina azikuseweletsa kwa ineyo sizoona (sizoona) Ukunzunzikiranji mkazi wokongola ngati iwe (mkazi wokongola ngati iwe) Mkazi wokongola ngati iwe (mkazi wokongola ngati iwe) Nde ukunzunzikiranji Nde ukunzunzikiranji Mayi inuyo anakonza (ah) Nde zoti wina azikuseweletsa kwa ineyo sizoona Nde ukunzunzikiranji mkazi wokongola ngati iwe (mkazi wokongola ngati iwe) Mkazi wokongola ngati iwe (mkazi wokongola ngati iwe) Nde ukunzunzikiranji Nde ukunzunzikiranji ♪ (Abstract)