Kishore Kumar Hits

Kelvin Sings - Mwana Uyu lyrics

Artist: Kelvin Sings

album: Mwana Uyu


Monga mwana wang'ono amadalila kholo
Kutsala yekha amakanitsitsa toto
Saayenda yekha angakagwele kumphopho
Kusangalatsa namalengaso ndi choncho
Osati matukutuku
Ngati ukukankha chikuku
Pamaso pamunthu wankulu
Osadutsa mukusuta ndudu
Chisomo chake ndichokwanila tonsefe
Chitsanzo ndi mwana wa Maria ndi yosefe
Pofunika mtanda wake tiwusenze
Chomwechi mpakana kumalembe
Poti iye ndi syllabus
Timulonde mapazi
Tisachite manyazi
Akationa nkumati
Mwana uyu uyu uyu
Mwana uyu uyu uyu
Ndiwanga aaa
Ndiwanga aaaa
Mwana uyu uyu uyu
Mwana uyu uyu uyu
Ndiwanga aaa
Ndiwanga aaaa
Ndifuna akandiona ine
A-zi-ti
Mwanayu ngwanga ine
Nde chitsanzo ndi nsembe
You'd think that he's a lannister
The way he paid my debt!!
Nde chili kwaine kufalitsa
Eeehe
Zachozizwa chomwe wachita
Eeehe
Nde kulikonse komwe nzapita
I'll represent CHRIST to the fullest wazizur?
Yeah
Ambuye anati mfana wopanda ntchito you need some company
Mu Aiguputo si Mo Salah upite Canaan
Ndipo, ankadziwa ndani mwala okanidwa uzaBuilder mfana ankakugendani
Posamila panga
Chitsime cha kuya koma posamila phwanga
Okontrola madzi mpaka osamila nkhwangwa
Kusintha mfana wa magazi othamanga kuposa MiRa mpaka
Timakuwa Abba Father
Amandipasa ma khatcha ndikayamba kudya machaka
Love yake jenuwini yosadyesana chi Banzi
Ine chimwemwe kutsaya nthawi zonse akamati
Mwana uyu uyu uyu
Mwana uyu uyu uyu
Ndiwanga aaa
Ndiwanga aaaa
Mwana uyu uyu uyu
Mwana uyu uyu uyu
Ndiwanga aaa
Ndiwanga aaaa

Поcмотреть все песни артиста

Other albums by the artist

Similar artists