Kishore Kumar Hits

Teddy Music - Mtima lyrics

Artist: Teddy Music

album: MAKADI


Ntima unasweka ndinkayesa nga wako ndiine ndekha
Zaka zitatu zongobetsa
Kundinamiza nnati ulipo wekha
Ndi Chikondi chakhathikhathi ndinakupatsa moyo wanga mosabwenza
Pano ntima uli madzi nsozi watsikila komwe unawubwenza
Kuti ukhale ntima mwanga
Sindingathe darli wanga
Wandipha mmoyo mwanga
Waupha ntima wanga
Kuti ukhale bwenzi langa
Sindingathe darli wanga
Wandipha mmoyo mwanga
Bwela Ndikuwuze
Za mu mtima (mu mtima)
Mu mtima (mu mtima)
Muntima mwanga mwadzadza revenge
Ndikufuna nditakhala ndi iwe koma muli mdima
(Muntima)
Muntima (muntima)
You told me you'd never cheat on me
Always you'll protect my heart
(Hhmm)
Pano nkakhala mmangoganizila if everything you said was lie
Unandiuza sunganditonze olo zitavuta maka
Pano anzanga onse akuwona uli ndi wina
Tell me how did you protect my pride
Kuti ukhale mmoyo mwanga
Sindingathe darli wanga
Waupha ntima wanga
Waupha ntima wanga
Waupha ntima wanga
Ndikuuze
Za mu mtima (mu mtima)
Mu mtima (mu mtima)
Muntima mwanga mwadzadza revenge
Ndikufuna nditakhala ndi iwe koma muli mdima
(Muntima)
Muntima (muntima)
(Muntima)
No matter what you say
No matter what you do
Makhalidwe ako andiwopsa
Mtima wangawu sukukhazikika
Ungomenya kuti bu bu bu
Bu bu bu bu bu
Ntima wungo gunda gunda gunda
Mmmhhmm hmm hmm hmm hmm
Menya kuti bu bu bu
Bu bu bu bu bu
Ntima wanga umango gunda
Mmmhhmm hmm hmm hmm hmm

Поcмотреть все песни артиста

Other albums by the artist

Similar artists