Inde anati kapilire Koma osati nkanamizire Kuti chikondi chipitilire Wandisandutsa wamasiye You always starting something Even when i do nothing Zofooka zanga usandutsa lupanga Khalidwe lakolo nde landiopsya Passive aggressive no more Masiku ake si anowa Chombo changa ndimanga Namondwe wamumtima mwanga Ndikamba Mtima nnapeleka wonse Nnawelengela ndi zala zonse I didn't know it'd be one of us That would tear us apart So hear from heart Za mu mtima (mu mtima) Mu mtima (mu mtima) Muntima mwanga mwadzadza revenge Ndikufuna nditakhala ndi iwe koma muli mdima (Muntima) Muntima (muntima) Remember how we used to kiss Every now and then by the beach You were my (Ride-ride-ride or die) You were my (Ride-ride-ride or die)