Amayo ine Mwana wanga ine Eeih aah mhu mhu mhu Eish koma ♪ Look amuna anga anapita Ndine single mom Chuma anandilanda achibale awo Anandisiyira mwana m'modzi yekha Love She's only 16 and she's all i have Kuti aphunzire school abale ndavutika Business ya makala kuyikapo mtima Bola masana okha angodyako nsima Alimbikire school adzandisunge patsogolo mwina Walimbikira wapita collage ya mankhwala Mayi ake asamadzavutike akangodwala Graduation ceremony yake ili pa mawa Ubwele kunyumba tidzamuthokoze Mulungu wanga Tili mkati mopemphera Mvula kugwa mpaka nyumba kutigwela Kukanika kumpulumutsa mwana madzi amutenga Nzamatsenga zitheka bwanji Ambuye mukundimvera? Ndidziwa misonzi yanu ndiyovuta kupuputa ih yeah Malingana ndi nyengo zomwe inu mudutsa ah hah ah hah Adziwa, Chauta wa mwamba Adziwa, kuliraku amamva Adziwa, mavuto amamva ah yeah eh eh eh Pain still fresh i'm asking where to smile Doesn't make sense at all to be alive Ambuye mwandisiya m'manja mwa adani If you really care about us where you are Pain still fresh i'm asking why to smile Doesn't make sense at all to be alive Ambuye mwandisiya m'manja mwa adani If you really care about us God then where you at? Yeah our faith is now shaking She got a lot of questions She fast to be strong on the other hand Being tempted to either wisdom from a serpent Mavuto amabweletsa maganizo oyipa Umayamba kuganiza anakakhala mwana wanzako Mavuto amabweletsa maganizoa awiri Kuyiwala Mulungu kapena kusendera kufupinaye I pray that God comforts you I'ts hard to believe that romans 8 it's so true sometimes I might just so leave it test To God make sense even when it doesn't make sense Ndidziwa misonzi yanu ndiyovuta kupuputa ih yeah Malingana ndi nyengo zomwe inu mudutsa ah hah ah hah Adziwa, Chauta wa mwamba Adziwa, kuliraku amamva Adziwa, mavuto amamva ah yeah eh eh eh