Kishore Kumar Hits

Lawi - Musawalange lyrics

Artist: Lawi

album: 30'S


Musawalange ondilakwira
Mukhululuke njira zawo (musawalange)
Oh-oh, musawalange iyayi
Musawalange ondilakwira
Mukhululuke njira zawo (musawalange)
Oh-oh, musawalange iyayi
Muli ndi chifundo, mumakhululuka
Mundikhululukirenso ine ndemwe
Chilungamo changa chili ngati nsanza
Munkupupuluma mwanga ndikukwiyitsani
Ndikukumbutsani mtanda
Ambuye wa chifundo
Pungulirani chiyero mwa ine
Ondilakwirawa muwapatse chikumbumtima ndi chikondi
Ndikuwalemba mu buku la moyo (musawalange)

Поcмотреть все песни артиста

Other albums by the artist

Similar artists