Njuchi Sting Ndinampeza Wondikonda opanda malire Ay yeah yeah Moni wakwana, a perfectionist Bandawe, (Bandawe) You wish you had me nawe, eya sungakane You had your time and i told you kulibeso wina ineyo Munali mukana searcher, a perfectionist Bandawe Ntchito yophweka bambo Ndimkati mundikonde bambo Mungondipatsa nthawi bambo You had your time and i told you kulibeso wina ineyo Ntchito yophweka bambo Ndimkati mundikonde bambo Mungondipatsa nthawi bambo He had his time and i told him, zibwanazi abetsa dona Pano mbiri yampeza Save the date yampeza Panopa news yampeza Invite yampeza Mbiri yampeza Save the date yampeza Panopa news yampeza Akuti fever yampeza Yampeza, mbiri Save the date, yampeza Invite yampeza Yampeza, mbiri Save the date, yampeza Akuti fever yampeza Sungavomeleze When i meet your fam amangoti ndinebe mula wawo Mpaka lero sadziwa zomwe anandipanga mwana wawo Shame on you, shame on you yeah Komwe uliko, komwe aliko Akumwa ma painkiller Life yabowa akumangolira Amandi caller ati adzimangilira, (ey yeah) Sizikusintha zaponda mwala Akumwa ma painkiller Life yabowa akumangolira Amandi caller ati adzimangilira, (koma) Sizikusintha zaponda mwala Pano mbiri yampeza Save the date yampeza Panopa news yampeza Invite yampeza Mbiri yampeza Save the date yampeza Panopa news yampeza Akuti fever yampeza Yampeza, mbiri Save the date, yampeza Invite yampeza Yampeza, mbiri Save the date, yampeza Akuti fever yampeza Mbiri yampeza Save the date yampeza Panopa news yampeza Invite yampeza Mbiri yampeza Save the date yampeza Panopa news yampeza Akuti fever yampeza ah Yeah Shame on you, shame on you yeah Because you never knew You never knew, you never knew Oh no Sispence on the board