Mmm zisunge, zisunge, zisunge Sende, sendee, sendela, sendelaa Patabadwa amuna angapo, ankafunabe mwana wa nkazi Mapemphero opanda yakho ndine ndemwe nthumazi Ndi ndi ndi ndiwe m'dalitso, Yankho ndiwe yankho The day they brought you home kunagwa mvula You are truly a miracle Maso angawa, ndaona zinthu maso angawa Imva ndamva zinthu makutu angawa The world is not a safe place for you nde dekha bae umve Zissuuuuunggeee You have a beautiful name with a beautiful future, Yankho uzisunge Zisuuuuunggeee You have a beautiful name You have a beautiful name Zisunge Zisunge Zisuuuuunggeee Zisunge You have a beautiful name You have a beautiful name Zisunge Sorry I wasn't home for your holiday Sorry I wasn't there for the new year Sorry for being a very busy brother, just like father Busy climbing up the ladder Mapemphero kumwamba, osayiwala Amen Ndimakukonda you are so special, dollar yawo akhale wa commercial Izakwana nthawi uzaziwa zosowa zako, uzazindikila mpavu ya ndalama Abale anzathu sangapange afford zonse, ndiyankhula zonse Izakwana nthawi yazinjoyi, nthawi yachikondi You are gonna be blinded ndi anzako ochepa omwewo ena sazakhala mbali yako Izakwana nthawi yosweka mtima, zinthu pena kuyenda, Pena kuyima But anyways you have a bright future, sindizalola kuti uzatayike I wanna see you fly high, Yolanda rule like a leader, J Banda Sindizalola uzikumbile manda, nzeru zako Yankho uzimangile mpanda Say no, know that you are priceless Say no Thupi lako simalonda Saay noo!! ndizakhumudwa ukazatayika Yankho Zissuuuuunggeee You have a beautiful name with a beautiful future, Yankho uzisunge Zisuuuuunggeee You have a beautiful name You have a beautiful name Zisunge Zisunge Zisuuuuunggeee Zisunge You have a beautiful name You have a beautiful name Zisunge Zisunge Zisunge Zisunge Zisunge