Hallelujah Coming in Ayyyah eh! Anakhalapo kusanakhale Analipo kuli palibe (ayy) Mpaka lero lino alipobe(Mpaka lero lino alipobe) Adzakhalapo mpakana kale(Adzakhalapo mpakana kale) Anandidziwa ine nsanabadwe(Anandidziwa ine nsanabadwe) Iwenso, follow me now(Iwenso, follow me now) Zaukulu wake ine ndiimba('iimba) Poti zonse ndilinazo nzake(nzake) Ngakhale ndine ochimwa amandikonda, amandikonda ah Ndikakhala pansi nkulingalila(Ndikakhala pansi nkulingalila) Kuyang'ana komwe ndachokela(Kuyang'ana komwe ndachokela) Ndimakweza manja nkumtama Namalenga(Ndimakweza manja nkumtama Namalenga) Poti ndi Yahweh Yahweh inu Poti ndi Yahweh Amandisunga, amandilera Ndati ndi Yahweh Yahweh inu Poti ndi Yahweh Amandisunga ine amandilela Uhmmmm Ayy Ndiye amene Amandisunga ine Uhmmmm Jehovah, ndiye Ndiye amane amandipatsa zonse ndisowa Monga M'busa wanga sindmasowa Chikondi chake Paine nchopanda cholowa Iye ndiwa Chaulele chosefukila ah He is more than a father More than just like a mother Iye ndoposa zonse zomwe dziko lipatsa He is more than a sister Than a friend and a brother Nouwooh Yahweh Poti ndi Yahweh Yahweh inu Poti ndi Yahweh Amandisunga, amandilera Ndati ndi Yahweh Yahweh inu Poti ndi Yahweh Amandisunga ine amandilela Ndikakhala pansi nkulingalila(uhmm uhmm) Kuyang'ana komwe ndachokela(uhmm uhmm) Ndimakweza manja nkumtama Namalenga