Nzanga ulibwanji? Zikuyenda bwanji? How is your family? Business ikuyenda bwanji? Poti dzikoli nde lavuta kwambiri On a daily, tikuluza fanz Kaya chaka chino zitithela bwanji Everyday kugwada pansi Mulungu akhululukire dziko la pansi Please hold on, my friend Stay strong, it's gonna be bumpy road I have hope, my friend We gonna be alright Koma pompano tikumana Tiyese kudzisamala Posachedwa kuwala Mwina tingodzisamala Osaopa nzanga Poti kukondwa ndi mawa Pompano kuwala We gonna dream of these days I miss those trips to the lake Zima boat ride uku tikusekelera Achina DJ Crips on the deck Tikuvina ndima cup tikumwe-mwelera Koma wapita-pita-pita-pita Tingosamalira mwina tidzawina Ayi-ah, ayi-ah ayi-ah, ayi-ah Tingosamalira mwina tidzawina Koma pompano tikumana Mwina tingodzisamala Posachedwa kuwala Tiyese kudzisamala Osaopa nzanga Poti kukondwa ndi mawa Pompano kuwala We gonna dream these days Ayi-ah, ayi-ah ayi-ah, ayi-ah Ayi-ah, ayi-ah ayi-ah, ayi-ah Ayi-ah, ayi-ah ayi-ah, ayi-ah Ayi-ah, ayi-ah ayi-ah, ayi-ah Yes, I miss church I miss family I miss being in the gym I miss hiking I miss those shows I miss you all Please stay safe, my friends