Yo Foxy Chi Piksy chimfana chodziwika ndi boma Zinayamba mwachibwana Ti ma show pa Gymkhana Ife tilibe chikwama Enawa ankatikana Kukwiya tikasanja Kumaseka tikanjanja Osalakwa kutilanga Kutiyang'anira under Kufeela ngati mlendo Kukhala ngati zoba opanda Frenzo Koma ndi chi hope kugwira ntchito Anawapanga mavuto onse history Ndeno Zikatere itsanana Tere itsanana Zikatere itsanana Zikatere itsanana Zikatere itsanana Tere itsanana Zikatere itsanana Zikatere itsanana Pano tiri ku mtunda Tikumatha kumajambura video kunja Zomwe sitikadyazo tikudya Sitiyenda pansi nde tili ndi nyumba Kale ankadutsa nkupita osatipatsa Moni Kuyimba osayankha phone Podutsa ma Ninja kuyika stones Pena ngati ungopita Joni Lero holiday(Namibia) Pop that champagne again(waziziwa) Sikuti nkufuna kunena kuti wandilira Uwu ndi umboni wanga mphwanga ndinashuphika Ndeno Zikatere itsanana Tere itsanana Zikatere itsanana Zikatere itsanana Zikatere itsanana Tere itsanana Zikatere itsanana Zikatere itsanana Uuuh Thank God for life Thank God for everything 'Cause paliponse pamene you are Aliponso wina wake amapafuna Hoooh Thank God for life Thank God for everything Cause paliponse pamene you are Aliponso wina wake amapafuna Tsono Zikatere itsanana Tere itsanana Zikatere itsanana Zikatere itsanana Zikatere itsanana Tere itsanana Zikatere itsanana Zikatere itsanana Zikatere itsanana Tere itsanananana Zikatere itsanana