Ngati umakonda undikonde ine
Ngati umakonda undikonde ine
Ndinangoti ayi
Ayi amama
Ndinagoti ayi
Ayi abambo
Ndinati zikomo
Zikomo malume
Komaso zikomo okonda wangayo
Ngati umakonda undikonde ine
Ngati umakonda undikonde ine
Pali ena amadziwa kukonda
Pali ena amadziwa kumvera
Pali ena amadziwa kukopa ooh
Chikondi chakale chosaona chuma
Chikondi chakale chisakangana
Komaso chakale chosakongola
Ndi mbiri zakale zonsezo zinatha
Ngati umakonda undikonde ine
Ngati umakonda undikonde ine
Pali ena amadziwa kukonda
Pali ena amadziwa kumvera
Pali ena ongodziwa kukopa
Ngati umakonda undikonde ine
Ngati umakonda undikonde ine
Ngati umadziwa undidziwe ine
Ngati umaona undione ine
Ngati umakonda undikonde ine
Ngati umadziwa undidziwe ine
Ngati umakonda undikonde ine
Ngati umaona undione ine
Ngati umakonda undikonde ine
Ngati umakonda undikonde ine
Ngati umadziwa undidziwe ine
Ngati umaona undione ine
Ndinangoti ayi
Ayi amama
Ndinangoti ayi
Ayi abambo
Ndinati zikomo
Zikomo malume
Komaso zikomo okonda wangayo
Поcмотреть все песни артиста
Other albums by the artist