Kishore Kumar Hits

MartseMw - Mkatimo lyrics

Artist: MartseMw

album: Mkatimo


Lero Nde tigona panjatu
Spice up ngati rajah
Akaziwa amatiwazatu
Mukununkhila Ndi mkatimo
Mukununkhila ndi mkatimo
Ndamva kwayatsidwa ganja
Ndamva kununkhila mkatimo
Ndabwera kudzaona nyanja
Koma mvuuu zili mkatimo
Ichi nde Ndi chi type changa
Ndichigoba ndichitchulila salimo
Musanditayitse time yanga man
Mukununkhila Ndi mkatimo
Nkhanga zanunkhiza ka dollar kanga kutumiza
Mukumachenjela mukachifukiza (ehem)
Ndisachite kukutupitsa
Mu ka hustle bagmo kukupisa
Ka donah kako kuphumitsa
Kukuteaser, kukuliza
Kukumenya nde kungokutchukitsa
Yakungana ya ma fazala
Khutu ngati chigoneleni chadzana
Ndabwera tokha ma guy sizomakana
Kukonda ngini izi zokha sindimakana
Change for what am in okay now
Kukometsa pa Malo
Zabwino sanena
My action men with a silencer

Поcмотреть все песни артиста

Other albums by the artist

Similar artists