Kishore Kumar Hits

Dr Namadingo - Mbili MalawiMusic lyrics

Artist: Dr Namadingo

album: Dr Namadingo


Ndili nayo mbili ineyo oh oh (zoona)
Ndakhalamo dziko lapansili (kwambili)
Ndavutikamo ine ndende yeah (zoona)
Ndagwilamo ntchito abale anga ine (zoona)
Koma yesu anandiombola (ineyo)
Koma yesu andiombola (ineyo)
Oh oh oh
Koma yesu anandiombola (ineyo)
Yesu wanga anandiwombola (ineyo)
Oh oh oh
Anthu ena mandithandiza ine (zoona)
Ndidayesetsa kulimbikila dekha (kwambili)
Kuti mwina ndidzithandize ineyo (zoona)
Ndipo Yesu sadangondilekelera (zoona)
Anakuza hema wanga ine (ineyo)
Anakuza hema wanga ine (ineyo)
Oh oh oh (yeah yeah yeah)
Anakuza malire anga ine (ineyo)
Anakuza malire anga ine (ineyo)
Oh oh oh (yeah yeah yeah!)
Oh salephere opeputsa dzina langa
Wondinyogodola singachite chabwino
Koma Yesu ndiye wandikoka ine eh eh
Wandiyika patsogolo ine
Wakulitsa hema wanga ine (ineyo)
Wakulitsa hema wanga ine (ineyo)
Oh oh oh
Wakulitsa malire anga ine (ineyo)
Wakulitsa malire anga ine (ineyo)
Oh oh oh (yeah yeah yeah!)
Aha ineyo
Wakulitsa malire anga ine (ineyo)
Oh oh oh (yeah yeah yeah!)
Wachotsa chitonzo changa ine (ineyo)
Wachoootsa! (ineyo)
Oh oh oh

Поcмотреть все песни артиста

Other albums by the artist

Similar artists