Kishore Kumar Hits

Lucius Banda - Chikhulupiliro lyrics

Artist: Lucius Banda

album: LOVE & HATE (The 20th and Final Release)


Ayi, wa, wa, wa, wa (eh)
Ma-ma-ma, oh-oh, oh
Ku painter ndi kutchena ndendende Beyonce (ndendende Beyonce)
Chinjale chako chokwera ndi Fortuner
Ma holiday Zanzbar, shopping Dubai
Champagne and cavier, kudya modula iwe
Koma zonse zili choncho
Udakapanganso chibwenzi
Kamnyamata kometa mbali, kopanda future
Lero mamuna'ko wamva, wakwiya, wapita
Kamnyamata kometa mbali kayamba kudumphadumpha
Chikondi ndili nacho mami (chikondi)
Koma chikhulupiliro yayi (oh)
Ngati munkathawira bwana ine ndi yani? (ayi)
Anakupatsa chilichonse awo (chilichonse)
Komabe unawaswera mtima
Chikamadya wina chilombo, mawa chidya ine (ine)
Chikondi ndili nacho mami (chikondi)
Koma chikhulupiliro yayi (oh)
Ngati munkathawira bwana ine ndi yani? (ayi)
Anakupatsa chilichonse awo (awo)
Komabe unawaswera mtima
Chikamadya wina chilombo, mawa chidya ine (ine)
Anapeza mamuna'ke ndi message ku WhatsApp (message ku WhatsApp)
M'malo mofufuza bwino, adangoti ndibwenzere
Lero banja lija latha, chilungamo wachiziwa
Message inali ya sister, "I love you so"
Two wrongs don't make it right
Kupunthwa sapikisana
Poti uzazindikira, mzako sanali olakwa
Pamene iwe ndiye, wataya ulemu wako onse
Kuli bwino kupusa pang'ono, mawa sunong'oneza bondo
Chikondi ndili nacho mami (chikondi)
Koma chikhulupiliro yayi (oh)
Ngati munkathawira bwana (bwana) ine ndi yani? (ayi)
Anakupatsa chilichonse awo (chilichonse)
Komabe unawaswera mtima
Chikamadya wina chilombo, mawa chidya ine (ine)
Chikondi ndili nacho mami (mami)
Koma chikhulupiliro yayi (oh)
Ngati munkathawira bwana ine ndi yani? (ayi)
Anakupatsa chilichonse awo (awo)
Komabe unawaswera mtima
Chikamadya wina chilombo, mawa chidya ine (ine)
Ndili ndi mantha (ndili nawo)
Ndili ndi mantha (ndimantha)
Ndili ndi mantha ineyo (ineyo)
Ndili ndi mantha (yeah)
Ndili ndi mantha (ndili ndi mantha)
Ndili ndi mantha (ndili ndi mantha)
Ndili ndi mantha ineyo (ineyo)
Ndili ndi mantha
Ndili ndi mantha (ndili ndi mantha)
Ndili ndi mantha (ndili ndi mantha)
Ndili ndi mantha ineyo
Ndili ndi mantha
Ndili ndi mantha (ndili ndi mantha)
Ndili ndi mantha (ndili ndi mantha)
Ndili ndi mantha ineyo (ndili ndi mantha)
Ndili ndi mantha

Поcмотреть все песни артиста

Other albums by the artist

Similar artists