Kishore Kumar Hits

Lucius Banda - Usaope Akachena lyrics

Artist: Lucius Banda

album: Time


Ooh oooh! oh oh
Ndiuze!
Kuyambira pomwe ndakuona
Mtima wanga sumakhala pansi
Ukaphoda mama ukathinitsa slit kusawutsa unyamata wanga
Ndikaganiza salary yanga
Zosowa zako sindingakwanitse
Ukamadutsa ndimangopenya
Window shopping, kukusilira
Tsiku lina udandipatsa chanza
Nkono wako utawulowolora
Tsiku lina udandisekelera
Za chikondi iwe pa ine umakayika
Kumayesa woku waver wina
Amene anali kumbuyo kwanga
Osadziwa umkandifuna
Koma poti mkazi sukanayankhura
Kuopa kuwoneka desperate
Koma sign yokha ukanandipatsa ooh oh
Ukanangophinya diso
Ukanangondinong'oneza iwe
Ukandikanga m'manja
Sindimkadziwa umandifuna
Amayi, musaope mkazi akatchena
Kutchenaku, ndimafuna inu mundikonde
Tingakongole bwanji
Tichisowa chikondi chabambo
Tingalemere bwanji
Sindingagule chikondi
Mai wawe ay ay ay ay oh
Mai wawe ay ay ay ay oh

Masiku ano zinthu zinasintha
Ndikale lomwe akazi anali pansi
Akazi ena lero ndizikhwaya
Zikuyendera range rover sport
Kukamuwona panyumba pake
Chilichonse ndicha England
Akasamba zodzoladzola
Iwe kugulitsa kugula ka vitz
Ungayambile pati kufusira?
Poti kenako ufusira ntchito
Sungadziwe ngati angakulore
Poyang'anira kulemera kwake
Umuyang'ane maso kwambiri
Udzawona misozi ya usiwa
Chomwe asowa ndi chikondi
Ngati wakukonda usaope nena
Sudziwa naye amakufuna
Koma monga mkazi sangayankhure ooh oh
Ukanangophinya diso
Ukanangondinong'oneza iwe
Ukandikanga m'manja
Sindimkadziwa umandifuna
Amayi, musaope mkazi akatchena
Kutchenaku, ndimafuna inu mundikonde
Tingakongole bwanji
Tichisowa chikondi chabambo
Tingalemere bwanji
Sindingagule chikondi
Mai wawe ay ay ay ay oh
Mai wawe ay ay ay ay oh

Mami-ma mami-ma
U-la-la-la ooh ooh ooh!
Whoa whoa!
(Ukanangophinya diso)
Ukanangophinya diso (ooh)
Ukanangondinong'oneza (nong'oneza weh)
Ukanandikanda m'manja (ooh)
Sindimkadziwa umandifuna
(Amayi)

Поcмотреть все песни артиста

Other albums by the artist

Similar artists