Haa! Mwayenda mtunda wotsiliza
Mwapita adadi inu
Bambo wanga ulendo inu
Ti-nkhani ndimva kwa yani?
Mume dadi mumtendere
Mwapita anzanga inu
Kuhewe kosakabwera
Pamtengo, mcheza ndi ndani?
Mupume mumtendere
Abambo alikonde
Ake si abwino
Aganiza, masiye wo bashi
Mwansiya ndekha ine
Ambuye, Parker Lilombe
Ambuye, Abisha Vunkoli
Enerst Chikakwiya oh oh
Kumtigo Ndileka Ndekha
Mdzafika kwathu ine
Mdzayimba limodzi ife
Mdzadika kwa bambo anga
Komwe kuli mpumulo
Komwe kulibe usiwa ndi njala
Komwe kulibe misonzi mkulira
Komwe kulibe inu nthenda ndi imfa
Komwe kuli abwezi wo
Anzanga, ndithu kundisiya
Abambo, kundusiya ndekha
Kani nawo abale nthawi imodzi
Muti ineyo mdzitani nanga?
Поcмотреть все песни артиста
Other albums by the artist