Kishore Kumar Hits

Lucius Banda - Tina lyrics

Artist: Lucius Banda

album: How Long?


Yo man ting a beatiful girl you know
Mr Lucius Banda and Sergio man once again
Highway productions man
Heheha
Kodi Tina ali konko?
Aah iye a likonko?
Mumuyitane ali konko
Aah iye a likonko? (eh wabwera)
Iwe Tina tabwera
Ndili ndi timawu
Ndikupita ku Lilongwe
Ndikafune ntchito
Undipatse chala Tina
Ndivekeko mphete
Kuti ikhale chikole cha chikondi changa
Ena amanena banja si ndalama
Koma ine nditi lero
Banja siumphawiso
Ndukafuna ndalama, tidzamange banja
Usazavutike Tina ndi umphawi wanga
Ndiwe okongola
Ndiwe okongola Tina
Ndiwe okongola undidikilire
Ndiwe okongola
Ndiwe okongola weche weche
Ndiwe okongola, undidikilire
Wakusalala, wakusalala Tina
Wakusalala, undidikilire
Wakusalala, perfume wapokopoko
Wakusalala undidikilire
Ndikuziwa kuti kwanu sunkadya therere
Tina ndiyesesa chonde kuti uzakondwe
Ndizakuchotsa ku Mangochi kunka Kumangoni
Uzasiya kudya nsomba uzizadya nyama
Akabwera amuna ozakufunsira
Uwaonetse mphete yanga
Uli pachibwenzi
Zina zimakhala nkhakamira za ma benz awo Tina
Udzikanitsitse mama
Zikhwaya zammangochi
Ndiwe okongola
Ndiwe okongola Tina
Ndiwe okongola undidikilire
Ndiwe okongola
Perfume weche weche
Ndiwe okongola, undidikilire
Wakusalala, wakusalala Tina
Wakusalala, undidikilire
Wakusalala, wakusalala weche weche
Wakusalala undidikilire
Kodi tina ulikumva iwe?
Ooh ulikumva?
Pomwe ndinena ulikumva iwe?
Aiye ulikumva?
Amuna ambiri lero ndi aulesi zedi
Angolowa m'banja alibe kalikonse
Mkazi akamamphe nyama
Ati okonda chuma
Usampute mwana waeni ulibe kalikonse
Pali akazi ena
Ndi wonyada udyo
Ndalama zandiwo mai
Kuthera kuziphoda
Kukongola kwa mkazi zikope ndizizi
Ndikugwira ntchito Tina ndikusekelera
Ndiwe okongola
Ndiwe okongola Tina
Ndiwe okongola, undidikilire
Ndiwe okongola
Perfume wapokopoko
Ndiwe okongola, undidikilire
Wakusalala, wakusalala Tina
Wakusalala undidikilire
Wakusalala, wakusalala wecheweche
Wakusalala, undidikilire
Iwetu Tina palibetu wina koma ndiwe wekha
Wawu wakusalala kwenjidyi kwangali
Wane ndi wawe mwina ndolite ey
Iwetu Tina palibetu wina koma ndiwe wekha
Wawu wakusalala kwenjidyi kwangali
Wane ndi wawe mwina ndolite ey
Once upon a time
In the year 2-G
Lucius Banda says you man
They must fit a far shine me know
Wind up your body and check your body girl
He's had a load out, you can't complain
Your face is so bright, your face is so shine
Like a moon in the sky, sine into the good things you know
Wind up your body and check your body girl
He's had a load out, you can't complain
Ndiwe okongola
Ndiwe okongola Tina
Ndiwe okongola undidikilire
Ndiwe okongola, perfume wa wecheweche
Ndiwe okongola undidikilire
Wakusalala, wakusalala Tina
Wakusalala undidikilire
Wakusalala, wakusalala wecheweche
Wakusalala undidikilire
Atopitopi ali konko
Ayi yeah ali konko
Alikonde ali konko
Ay yeah ali konko
A Boniface muli konko inu?
Ooh oh ali konko
(A Banda muli konko?)
(Ay yeah muli konko)

Поcмотреть все песни артиста

Other albums by the artist

Similar artists